Ndandanda ya Mlungu wa January 17
MLUNGU WOYAMBIRA JANUARY 17
Nyimbo Na. 35 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cf mutu 1 ndime 8-15 (Mph. 25)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Ezara 1-5 (Mph. 10)
Na. 1: Ezara 3:1-9 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: N’chifukwa Chiyani Ayuda Ambiri Sanavomereze Kuti Yesu Ndi Mesiya?—rs tsa. 425 ndime 1 ndi 2 (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Mzimu umabwerera Motani kwa Mulungu?—Mlal. 12:7 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 10: Kufunika Kobwereza Mfundo Mu Utumiki Wakumunda. Nkhani yokambirana yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki tsamba 206 mpaka 207. Chitani chitsanzo chachidule chosonyeza mmene tingagwiritsire ntchito mfundo imodzi kapena ziwiri za m’nkhaniyi.
Mph. 20: “Kodi Mukudziwa Zimene Mungasankhe?” Mafunso ndi mayankho. Pofotokoza mawu oyamba, gwiritsani ntchito ndime 1 ndipo m’mawu anu omaliza tchulani mfundo za mu ndime 3. Nkhani yokambidwa ndi mkulu.
Nyimbo Na. 7 ndi Pemphero