Ndandanda ya Mlungu wa January 31
MLUNGU WOYAMBIRA JANUARY 31
Nyimbo Na. 30 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cf mutu 2 ndime 1-8 (Mph. 25)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Nehemiya 1-4 (Mph. 10)
Na. 1: Nehemiya 2:11-20 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: Kodi Lemba la Yohane 1:1 Limatsimikizira Kuti Yesu ndi Mulungu?—rs tsa. 426 ndime 4 mpaka tsa. 427 ndime 1 (Mph. 5)
Na. 3: Zimene Tingachite Potsatira Mawu a Yesu a pa Mateyu 22:21 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 20: “Mphatso Yothandiza Kwa Mabanja.”—Gawo 2. (Ndime 7-13) Mafunso ndi mayankho. Pemphani omvera kufotokoza mmene mabanja awo apindulira pogwiritsa ntchito mfundo zina zomwe zili pa tsamba 6.
Mph. 10: “Phunzitsani Ana Anu Kuti Adzakhale Atumiki.” Mafunso ndi mayankho. Pemphani omvera kuti afotokoze njira zimene makolo awo anawathandizira kuti akhale ndi zolinga mu utumiki komanso kuyesetsa kuzikwaniritsa.
Nyimbo Na. 41 ndi Pemphero