Ndandanda ya Mlungu wa March 7
MLUNGU WOYAMBIRA MARCH 7
Nyimbo Na. 28 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cf mutu 3 ndime 20-24 ndi bokosi patsamba 34 (Mph. 25)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Esitere 6–10 (Mph. 10)
Na. 1: Esitere 7:1-10 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: Kodi Chifukwa Chakuti Ena Amagwadira Yesu, Ndiye Kuti Iye Ndi Mulungu?—rs tsa. 429 ndime 1 mpaka 3 (Mph. 5)
Na. 3: N’chifukwa chiyani Yesu Ali Mtumiki Wamkulu Ndiponso Wokwaniritsa Chikhulupiriro Chathu?—Aheb. 12:2 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 10: Muziphunzitsa Mokopa. Nkhani yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, tsamba 255 ndi 257. Chitani chitsanzo chachidule chosonyeza mmene mungagwiritsire ntchito mfundo imodzi kapena ziwiri za mu nkhaniyi.
Mph. 10: Muzigwiritsa Bwino Ntchito Timapepala. Nkhani yokambirana. Tchulani timapepala timene tilipo m’chinenero chanu. Fotokozani nthawi imene mungagawire timapepalato ndiponso fotokozani n’chifukwa chiyani mukuona kuti anthu angachite nato chidwi. Pemphani omvera kuti afotokoze zimene zawathandiza kuti azigwiritsa ntchito bwino timapepala. Chitani chitsanzo chimodzi kapena ziwiri.
Mph. 10: Zosowa za pampingo.
Nyimbo Na. 35 ndi Pemphero