Ndandanda ya Mlungu wa May 2
MLUNGU WOYAMBIRA MAY 2
Nyimbo Na. 30 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cf mutu 6 ndime 10-18 (Mph. 25)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Yobu 38-42 (Mph. 10)
Na. 1: Yobu 40:1-24 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: Ubwino Wokhala Munthu Wofatsa Ndiponso Woleza Mtima (Mph. 5)
Na. 3: Ngati Wina Anena Kuti: “Kodi Mumavomereza Yesu Kukhala Mpulumutsi Wanu?”—rs tsa. 433 ndime 4 mpaka tsa. 434 ndime 1 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 3: Zilengezo.
Mph. 9: Zindikirani Maganizo a Wofunsayo. Nkhani yokambirana yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, tsamba 66 mpaka tsamba 68 ndime 3.
Mph. 15: Zosowa za pampingo.
Mph. 8: Konzekerani Kugawira Magazini M’mwezi wa May. Nkhani yokambirana. Fotokozani zimene zili m’magaziniwo kwa mphindi imodzi kapena ziwiri. Kenako sankhanimo nkhani ziwiri kapena zitatu, ndipo funsani omvera kuti anene mafunso ndi malemba amene tingagwiritse ntchito pogawira magaziniwo. Chitani zitsanzo zosonyeza mmene tingagawirire magazini iliyonse.
Nyimbo Na. 51 ndi Pemphero