Ndandanda ya Mlungu wa June 6
MLUNGU WOYAMBIRA JUNE 6
Nyimbo Na. 17 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cf mutu 8 ndime 1-9 (Mph. 25)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Masalimo 34-37 (Mph. 10)
Na. 1: Salimo 35:1-18 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: Kodi Zimene Zikuchitika ku Isiraeli Masiku Ano Zikukwaniritsa Ulosi wa M’Baibulo?—rs tsa. 45 ndime 1 mpaka tsa. 46 ndime 2 (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Tikuphunzira Chiyani pa Luka 12:13-15, 21? (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo. Fotokozani nkhani yakuti, “Kulemekeza Yehova Ndi Zinthu Zathu Zamtengo Wapatali.”
Mph. 10: Gwiritsani Ntchito Mafunso Kuti Muziphunzitsa Mogwira Mtima: Gawo 2. Nkhani yokambirana yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, tsamba 237 ndime 3 mpaka tsamba 238 ndime 5. Chitani chitsanzo chachidule chosonyeza mmene mungagwiritsire ntchito mfundo imodzi kapena ziwiri za m’nkhaniyo.
Mph. 10: Zosowa za pampingo.
Mph. 10: Kodi Tinachita Zotani? Nkhani yokambirana yokambidwa ndi woyang’anira utumiki. Yamikirani mpingo chifukwa cha zimene unachita pa nyengo ya Chikumbutso ndipo fotokozani zotsatira zake. Pemphani omvera kuti afotokoze zinthu zosangalatsa zimene anakumana nazo pochita upainiya wothandiza m’miyezi ya March, April ndi May.
Nyimbo Na. 52 ndi Pemphero