Ndandanda ya Mlungu wa October 22
MLUNGU WOYAMBIRA OCTOBER 22
Nyimbo Na. 43 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
bt mutu 14 ndime 1-5 ndi bokosi patsamba 112 (Mph. 30)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Hoseya 1-7 (Mph. 10)
Na. 1: Hoseya 6:1-10 ndi 7:1-7 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: Kodi Mbali ya Padziko Lapansi ya Gulu la Yehova Tingaidziwe Bwanji?—rs tsa. 143 ndime 1-7 (Mph. 5)
Na. 3: Tsanzirani Yesu Ndipo Musamaope Kuchita Manyazi—Aheb. 12:2 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 30: Zimene Achinyamata Amadzifunsa—Kodi Ndingapeze Bwanji Anzanga Enieni? Mafunso ndi mayankho. Nkhani yochokera mu Galamukani! ya March 2009, tsamba 18 mpaka 20. Gwiritsani ntchito mfundo za m’ndime yoyamba ndi yomaliza monga mawu oyamba ndi omaliza. Ngati nthawi ilipo, werengani ndi kukambirana malemba amene ali m’nkhaniyi.
Nyimbo Na. 89 ndi Pemphero