Ndandanda ya Mlungu wa November 12
MLUNGU WOYAMBIRA NOVEMBER 12
Nyimbo Na. 118 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
bt mutu 15 ndime 1-7 ndi bokosi patsamba 116 (Mph. 30)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Amosi 1-9 (Mph. 10)
Na. 1: Amosi 3:1-15 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: Kodi “Chipangano Chatsopano” Chimanena Kuti Dziko Lapansi Lidzakhala Paradaiso Ngati Mmene “Chipangano Chakale” Chimanenera?—rs tsa. 336 ndime 1-3 (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Kumvetsa Bwino Lemba la Salimo 51:17 Kungatithandize Bwanji? (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph 10: Ngati Wina Atanena Kuti, ‘Simumakhulupirira Yesu.’ Nkhani yokambirana yochokera m’buku la Kukambitsirana tsamba 433, ndime 1 mpaka 3. Chitani chitsanzo chimodzi chachidule.
Mph 10: Kodi Tikuphunzirapo Chiyani? Nkhani yokambirana. Werengani Maliko 1:16-20. Kambiranani mmene malemba amenewa angatithandizire mu utumiki wathu.
Mph 10: “Muzisangalala Chifukwa Chogwira Ntchito Mwakhama.” Mafunso ndi mayankho.
Nyimbo Na. 98 ndi Pemphero