Ndandanda ya Mlungu wa December 17
MLUNGU WOYAMBIRA DECEMBER 17
Nyimbo Na. 101 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
bt mutu 16 ndime 8-12, ndi bokosi patsamba 132 (Mph. 30)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Zekariya 1-8 (Mph. 10)
Na. 1: Zekariya 8:1-13 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: Kodi Tingasonyeze Bwanji Kuti Yehova Ndi Ambuye Wamkulu Koposa?—Sal. 73:28 (Mph. 5)
Na. 3: N’chifukwa Chiyani Anthu Oganiza Bwino Amaphunzira Zimene Yesu Khristu Ankaphunzitsa, M’malo Mwa Nzeru za Anthu?—rs tsa. 138 ndime 1–tsa. 139 ndime 1 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: “Zimene Munganene Pogawira Magazini mu . . .” Nkhani yokambirana.
Mph. 10: Uthenga Umene Tiyenera Kulengeza—“Opani Mulungu Woona, Sungani Malamulo Ake.” Nkhani yokambidwa mwa umoyo yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki tsamba 272 mpaka pakamutu kamene kali patsamba 275.
Mph. 15: Kodi Mwaiyesa? Nkhani yokambirana. Kambani nkhani yofotokoza mfundo zachidule zopezeka m’nkhani zotsatirazi zopezeka mu Utumiki Wathu wa Ufumu waposachedwapa. Nkhani zake ndi zakuti: “Muzilalikira Molimba Mtima Kumalo a Ntchito ndi Amalonda” (km 3/12), “Thandizani Anthu Kumvera Mulungu” (km 7/12), ndi “Yesetsani Kumalalikira Madzulo?” (km 10/12). Pemphani omvera kufotokoza mmene kugwiritsa ntchito mfundo zopezeka m’nkhanizi kwawathandizira.
Nyimbo Na. 117 ndi Pemphero