Ndandanda ya Mlungu wa July 29
MLUNGU WOYAMBIRA JULY 29
Nyimbo Na. 49 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
bt mutu 26 ndime 16-22 ndi bokosi patsamba 209 (Mph. 30)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Machitidwe 26–28 (Mph. 10)
Na. 1: Machitidwe 26:19-32 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: Kodi Akhristu Okhulupirika Adzatengedwa Kupita Kumwamba Mobisa Asanafe?—rs tsa. 215 ndime 2 mpaka tsa. 216 ndime 1 (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Tingadziwe Bwanji Kuti Mzimu Woyera wa Mulungu Ukugwira Ntchito mwa Atumiki Ake?—Agal. 5:22, 23; Chiv. 22:17 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 10: Kulankhula Mwachibadwa Polalikira. Nkhani yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, tsamba 128 ndime 1, mpaka tsamba 129 ndime 1. Mwachidule, funsani wofalitsa mmodzi kuti afotokoze zimene zinamuthandiza kuthetsa manyazi mu utumiki.
Mph. 10: Bokosi la Mafunso. Nkhani yokambirana yokambidwa ndi mkulu.
Mph. 10: Sonyezani Kuti Ndinudi Ana a Atate Wanu Wakumwamba. (Mat. 5:43-45) Nkhani yochokera mu Buku Lapachaka la 2013, tsamba 89 ndime 3, mpaka tsamba 90 ndime 1, ndi tsamba 164 ndime 2. Pemphani omvera kuti afotokoze zimene tikuphunzirapo.
Nyimbo Na. 80 ndi Pemphero