Ndandanda ya Mlungu wa September 30
MLUNGU WOYAMBIRA SEPTEMBER 30
Nyimbo Na. 81 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
jr mutu 1 ndime 15-21 (Mph. 30)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Agalatiya 1-6 (Mph. 10)
Na. 1: Agalatiya 1:18-24 mpaka 2:1-10 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: N’chifukwa Chiyani Pali Zipembedzo Zambiri?—rs tsa. 83 ndime 1-tsa. 84 ndime 2 (Mph. 5)
Na. 3: N’chifukwa Chiyani Yehova Ali Woyenera Kulambiridwa?—Chiv. 4:11 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 10: “Amenewanso Muziwaganizira.” Nkhani yokambirana. Chitani chitsanzo chosonyeza mmene mungayambitsire phunziro Loweruka loyambirira m’mwezi wa October.
Mph. 10: Njira Zolalikirira Uthenga Wabwino—Kulalikira Kwa Anthu a Zinenero Zonse. Nkhani yokambirana yochokera m’buku la Gulu, tsamba 104, ndime 2, mpaka tsamba 105, ndime 3. Chitaninso chitsanzo.
Mph. 10: Musadere Nkhawa. (Mat. 6:31-33) Nkhani yokambirana yochokera mu Buku Lapachaka la 2013, patsamba 138, ndime 3, mpaka tsamba 139, ndime 3. Pemphani omvera kuti anene zimene aphunzira pa nkhaniyo.
Nyimbo Na. 40 and Pemphero