Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 4/14 tsamba 4
  • Ndandanda ya Mlungu wa May 5

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa May 5
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2014
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA MAY 5
  • Mph. 10: Zosowa za pampingo.
Utumiki Wathu wa Ufumu—2014
km 4/14 tsamba 4

Ndandanda ya Mlungu wa May 5

MLUNGU WOYAMBIRA MAY 5

Nyimbo Na. 123 ndi Pemphero

Phunziro la Baibulo la Mpingo:

jr mutu 11 ndime 1-8 (Mph. 30)

Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: Ekisodo 23-26 (Mph. 10)

Na. 1: Ekisodo 25:1-22 (Osapitirira mph. 4)

Na. 2: M’Baibulo Palibe Pamene Panalembedwa Kuti Adamu Ankasunga Sabata—rs tsa. 346 ndime 4–tsa. 347 ndime 2 (Mph. 5)

Na. 3: Kodi Kukhulupirira Mizimu N’kutani?—bh tsa. 100-103 ndime 10-13 (Mph. 5)

Msonkhano wa Utumiki:

Nyimbo Na. 117

Mph. 10: Zimene Munganene Pogawira Magazini a May. Nkhani yokambirana. Yambani ndi kuchita chitsanzo cha mmene tingagawirire magaziniwo pogwiritsa ntchito zitsanzo za ulaliki zimene zili patsamba lino. Kenako kambiranani zitsanzozo, kuyambira poyamba mpaka pamapeto. Chitani zimenezi mpaka mutamaliza kuwerenga mawu onse. Pomaliza, limbikitsani ofalitsa onse kuti awerenge magaziniwo n’cholinga choti awadziwe bwino komanso alimbikitseni kuti adzagawire nawo magaziniwa.

Mph. 10: Zosowa za pampingo.

Mph. 10: Kodi Tinachita Zotani? Nkhani yokambirana. Pemphani omvera kuti afotokoze mmene anapindulira pogwiritsa ntchito malangizo a m’nkhani yakuti, “Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki—Muzithandiza Mnzanu Amene Mwayenda Naye.” Kenako apempheni kuti anene zinthu zosangalatsa zimene anakumana nazo.

Nyimbo Na. 103 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena