Ndandanda ya Mlungu wa June 16
MLUNGU WOYAMBIRA JUNE 16
Nyimbo Na. 77 ndi Pemphero
Phunziro la Baibulo la Mpingo:
jr mutu 12 ndime 20-25 ndi bokosi patsamba 151 (Mph. 30)
Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Levitiko 6-9 (Mph. 10)
Na. 1: Levitiko 8:18-30 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: Chifukwa Chimene Sitipemphera kwa “Oyera Mtima”—rs tsa. 332 ndime 2-4 (Mph. 5)
Na. 3: N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuvala Bwino Tikamachita Utumiki Wakumunda Kapena Kumisonkhano Yachikhristu?—lv tsa. 57 ndime 14-15 (Mph. 5)
Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 30: “Kodi Mukudziwa Zimene Mungasankhe?” Mafunso ndi mayankho. Gwiritsani ntchito mfundo zomwe zili m’ndime yoyamba ngati mawu oyamba ndipo zimene zili m’ndime yachitatu ngati mawu omaliza. Mukambiranenso tsamba 215 mpaka 217 m’buku la Chikondi cha Mulungu. Limbikitsani ofalitsa onse obatizidwa kuti akamayenda, nthawi zonse azitenga khadi la DPA. Ikambidwe ndi mkulu woyenerera.
Nyimbo Na. 120 ndi Pemphero