Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 2/15 tsamba 1
  • Ndandanda ya Mlungu wa February 9

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa February 9
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2015
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA FEBRUARY 9
Utumiki Wathu wa Ufumu—2015
km 2/15 tsamba 1

Ndandanda ya Mlungu wa February 9

MLUNGU WOYAMBIRA FEBRUARY 9

Nyimbo Na. 24 ndi Pemphero

Phunziro la Baibulo la Mpingo:

cl mutu 8 ndime 9-16 (Mph. 30)

Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: Oweruza 11-14 (Mph. 8)

Na. 1: Oweruza 13:15-25 (Osapitirira mph. 3)

Na. 2: Kodi Angelo Amatithandiza Bwanji Tikamalalikira?​—bt tsa. 58-59 ndime 16-18 (Mph. 5)

Na. 3: Kodi Baibulo Ndi Lolondola pa Nkhani Zasayansi?​—igw tsa. 7 ndime 1-3 (Mph. 5)

Msonkhano wa Utumiki:

Mutu wa Mwezi Uno: Khalani “Odzipereka pa Ntchito Zabwino”​—Tito 2:14.

Nyimbo Na. 54

Mph. 15: “N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kukhala ‘Odzipereka pa Ntchito Zabwino’?” Nkhani yokambirana. Kambirananinso mfundo zomwe zikupezeka mu Nsanja ya Olonda ya June 1, 2002 tsamba 23 ndime 17-19.

Mph. 15: “Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki​—Kulalikira Pogwiritsa Ntchito Intakomu Kapena M’madera a Chitetezo Chokhwima.” Nkhani yokambirana. Kambiranani zitsanzo za mu Yearbook ya 2011 ndi ya 2000 zomwe zili mu nkhaniyi. Kenako pemphani omvera kuti anene zimene anakumana nazo pamene ankalalikira munthu wachidwi pogwiritsa ntchito intakomu, foni kapena kalata. Angafotokozenso zimene anakumana nazo pamene ankalalikira m’madera a chitetezo chokhwima kapena m’dera la nyumba za mipanda. Pa mfundo zomwe zatchulidwa m’nkhaniyi, tsindikani zomwe zikugwirizana ndi gawo lanu. Chitani chitsanzo chosonyeza mmene tingagwiritsire ntchito mfundo zomwe zili m’nkhaniyi.

Nyimbo Na. 33 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena