Ndandanda ya Mlungu wa June 1
MLUNGU WOYAMBIRA JUNE 1
Nyimbo Na. 69 ndi Pemphero
Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cl mutu 13 ndime 19-23 ndi bokosi patsamba 137 (30 min.)
Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: 2 Samueli 16-18 (8 min.)
Na. 1: 2 Samueli 17:14-20 (Osapitirira 3 min.)
Na. 2: Kodi Tikuphunzira Chiyani pa Mkangano wa Paulo ndi Baranaba?—bt tsa. 119-120 ndime 8-11 (5 min.)
Na. 3: Kodi Mungatani Kuti Muzigwiritsa Ntchito Bwino Ndalama?—igw tsa. 21 ndime 1-4 (5 min.)
Msonkhano wa Utumiki:
Mutu wa Mwezi Uno: Muzithandiza anthu onse kudziwa choonadi molondola.—1 Tim. 2:3, 4.
10 min: Zimene Munganene Pogawira Magazini a June. Nkhani yokambirana. Yambani ndi kuchita chitsanzo chosonyeza zimene tinganene pogawira magaziniwa pogwiritsa ntchito zitsanzo zaulaliki zomwe zili patsamba lino. Kenako kambiranani chitsanzo cha ulaliki chilichonse kuyambira poyambirira mpaka pamapeto.
10 min: Zofunika pampingo.
10 min: Kodi Tinachita Zotani? Nkhani yokambirana. Pemphani omvera kuti afotokoze mmene anapindulira ndi mfundo zomwe zili munkhani yakuti, “Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki—Muzilalikira Anthu Oyankhula Chinenero China.” Kenako apempheni kuti afotokoze zinthu zosangalatsa zomwe anakumana nazo.
Nyimbo Na. 25 ndi Pemphero