Zilengezo
◼ Mabuku ogawira mu May ndi June: Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? kapena kapepala kakuti, Kodi Mukufuna Kudziwa Choonadi? July ndi August: Mverani Mulungu, Mverani Mulungu Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha ndi kakuti, Uthenga Wabwino Wochokera kwa Mulungu.