Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 6/15 tsamba 2
  • Ndandanda ya Mlungu wa June 15

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa June 15
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2015
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA JUNE 15
Utumiki Wathu wa Ufumu—2015
km 6/15 tsamba 2

Ndandanda ya Mlungu wa June 15

MLUNGU WOYAMBIRA JUNE 15

Nyimbo Na. 8 ndi Pemphero

Phunziro la Baibulo la Mpingo:

cl mutu 14 ndime 10-15 (30 min.)

Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: 2 Samueli 22–24 (8 min.)

Na.  1: 2 Samueli 22:21-32 (Osapitirira 3 min.)

Na.  2: Kodi Timatani Tikapatsidwa Malangizo?—Gen. 4:6-11 (5 min.)

Na.  3: Timasangalala Tikakhala Achikondi Ndiponso Omvera—igw tsa. 22 ndime 4-6 (5 min.)

Msonkhano wa Utumiki:

Mutu wa Mwezi Uno: “Kumbukirani masiku akale”—Deut. 32:7.

Nyimbo Na. 88

12 min: Kodi Ndi Munthu Uti wa M’Baibulo Amene Nkhani Yake Imakuchititsani Chidwi? Kufunsa komanso nkhani. Yambani ndi kufunsa ana awiri kapena atatu mafunso otsatirawa. Kodi ndi munthu uti wotchulidwa m’Baibulo amene amamukonda kwambiri? Kodi munthu ameneyu anachita chiyani? Kodi angamutsanzire bwanji? Kenako kambani nkhani. Fotokozani mmene ana angapindulire ndi makadi a anthu otchulidwa m’Baibulo omwe akupezeka pa jw.org/ny. (Pitani pamene palembedwa kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANA.) Kakhadi kalikonse kali ndi chithunzi, kamafotokoza za munthuyo, mapu a kumene ankakhala, nthawi imene anakhala ndi moyo komanso mafunso atatu ndi mayankho ake. Mukhoza kukopera, kusindikiza komanso kusunga kakhadi kalikonse. Limbikitsani makolo amene ali ndi ana aang’ono kuti azigwiritsa ntchito timakadi timeneti pophunzitsa ana awo zinthu za “masiku akale.” (Deut. 32:7) Ngati kwanuko mulibe mwayi wogwiritsa ntchito intaneti kambani nkhaniyi pogwiritsa ntchito Bukhu Langa la Nkhani za Baibulo.

18 min: “Tiziphunzira kwa Ofalitsa Aluso.” Nkhani yokambirana. Mukamaliza kukambirana ndime yachiwiri, pemphani omvera kuti afotokoze zinthu zothandiza zimene anaphunzira atalowa mu utumiki ndi wofalitsa waluso.

Nyimbo Na. 4 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena