Zilengezo
◼ Mabuku ogawira mu December: Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? kapena timapepala totsatirati: Kodi Baibulo Mumalikhulupirira?, Kodi Dziko Lapansili Lili M’manja mwa Ndani?, Kodi Mavuto Amene Tikukumana Nawowa Adzathadi?, Kodi Mukuganiza Kuti Zinthu Zidzakhala Bwanji M’tsogolo?, Kodi N’chiyani Chingathandize Kuti Banja Likhale Losangalala? Kodi Ufumu wa Mulungu N’chiyani? ndi kakuti, Kodi N’zoonadi Kuti Akufa Adzauka? January ndi February 2016: Timabuku takuti, Mverani Mulungu, Mverani Mulungu Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha ndi kakuti Uthenga Wabwino Wochokera kwa Mulungu. March: Magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani!