Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 February tsamba 4
  • February 15-21

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • February 15-21
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 February tsamba 4

February 15-21

NEHEMIYA 9-11

  • Nyimbo Na. 84 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Anthu Okhulupirika Amatsatira Malangizo a Gulu la Yehova”: (10 min.)

    • Neh. 10:28-30—Anamvera zoti asakwatirane ndi “anthu a m’mayikowo” (w98 10/15 21 ndime 11)

    • Neh. 10:32-39—Iwo anatsimikiza kuti azithandiza pa kulambira koona (w98 10/15 21 ndime 11-12)

    • Neh. 11:1, 2—Anamvera ndi mtima wonse malangizo a gulu la Yehova (w06 2/1 11 ndime 6; w98 10/15 22 ndime 13)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Neh. 9:19-21—Kodi Yehova anasonyeza bwanji kuti amapereka kwa anthu ake zinthu zofunika? (w13 9/15 9 ndime 9-10)

    • Neh. 9:6-38—Kodi Alevi anapereka chitsanzo chotani pa nkhani yopemphera? (w13 10/15 22-23 ndime 6-7)

    • Kodi ndaphunzira chiyani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: Neh. 11:15-36 (Osapitirira 4 min.)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gawirani Galamukani! yatsopano pogwiritsa ntchito mutu wakuti “Mfundo Zothandiza Mabanja—Kodi Mungatani Kuti Mukhale ndi Anzanu Apamtima?” Muuzeni zimene mudzakambirane mukadzabweranso.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Chitani chitsanzo chosonyeza ulendo wobwereza kwa munthu amene anasangalala ndi mutu wakuti “Mfundo Zothandiza Mabanja—Kodi Mungatani Kuti Mukhale ndi Anzanu Apamtima?” Muuzeni nkhani yomwe mudzaphunzire mukadzabweranso.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) Chitani chitsanzo chosonyeza mukuphunzira ndi munthu. (bh 32-33 ndime 13-14)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 19

  • “Moyo Wabwino Kwambiri”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Yambani ndi kuonetsa vidiyo. Kenako kambiranani mafunso. Funsani wofalitsa mmodzi yemwe ali pabanja kapena amene sali pabanja yemwe wachita zambiri potumikira Yehova asanalowe m’banja. (1 Akor. 7:35) Kodi anadalitsidwa bwanji?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: cl mutu 26 ndime 1-9 (30 min.)

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 76 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena