Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 March tsamba 2
  • March 7-13

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • March 7-13
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 March tsamba 2

March 7-13

ESITERE 6-10

  • Nyimbo Na. 131 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Esitere Anasonyeza Kuti Sanali Wodzikonda”: (10 min.)

    • Esitere 8:3, 4—Esitere anaika moyo wake pangozi pofuna kuthandiza anthu ena (ia 143 ndime 24-25)

    • Esitere 8:5—Esitere anayankhula ndi Ahasiwero mwanzeru (w06 3/1 11 ndime 8)

    • Esitere 8:17—Anthu ambiri anayamba kutsatira chipembedzo cha Ayuda (w06 3/1 11 ndime 3)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Esitere 8:1, 2—Kodi ulosi umene Yakobo ananena atatsala pang’ono kufa wakuti ‘madzulo Benjamini adzagawa zimene wafunkha,’ unakwaniritsidwa bwanji? (ia 142, bokosi)

    • Esitere 9:10, 15, 16—N’chifukwa chiyani Ayuda sanalande zofunkha ngakhale kuti lamulo linawalola kuchita zimenezi? (w06 3/1 11 ndime 4)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: Esitere 8:1-9 (Osapitirira 4 min.)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Kukonzekera Ulaliki wa Mwezi Uno: (15 min.) Nkhani yokambirana. Pambuyo poonetsa vidiyo ya chitsanzo cha ulaliki iliyonse payokha, kambiranani mfundo zimene mwaphunzirapo. Kenako kambiranani nkhani yakuti, “Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki—Kukonza Ulaliki Wanuwanu wa Magazini.”

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 118

  • “Tidzalandire Bwino Alendo”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Pemphani ofalitsa kuti afotokoze zinthu zabwino zimene zinachitika chifukwa cholandira bwino alendo pa Chikumbutso cha chaka chatha. Chitani chitsanzo chosonyeza zinthu zabwino zimene zinachitika.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: cl mutu 27 ndime 1-9 (30 min.)

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 147 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena