Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 March tsamba 4
  • March 14-20

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • March 14-20
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 March tsamba 4

March 14-20

YOBU 1-5

  • Nyimbo Na. 89 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yobu Anakhalabe Wokhulupirika Pamene Ankayesedwa”: (10 min.)

    • [Onetsani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Yobu.]

    • Yobu 1:8-11—Satana ananena kuti Yobu ankatumikira Mulungu ndi zolinga zoipa (w11 5/15 17 ndime 6-8; w09 4/15 3 ndime 3-4)

    • Yobu 2:2-5—Satana ananena kuti anthu satumikira Mulungu ndi zolinga zabwino (w09 4/15 4 ndime 6)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yobu 1:6; 2:1​—Kodi ndi ndani amene ankaloledwa kukaonekera kwa Yehova? (w06 3/15 13 ndime 6)

    • Yobu 4:7, 18, 19—Kodi ndi zinthu zabodza ziti zimene Elifazi anauza Yobu? (w14 3/15 13 ndime 3; w05 9/15 26 ndime 4-5; w95 2/15 27 ndime 5-6)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: Yobu 4:1-21 (Osapitirira 4 min.)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: wp16.2 tsamba loyamba—Muuzeni nkhani imene mudzakambirane ulendo wotsatira. (Osapitirira 2 min.)

  • Ulendo Wobwereza: wp16.2 tsamba loyamba—Muuzeni nkhani imene mudzaphunzire ulendo wotsatira. (Osapitirira 4 min.)

  • Phunziro la Baibulo: fg phunziro 2 ndime 2-3 (Osapitirira 6 min.)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 88

  • Musamangotengera Zochita za Anzanu: (15 min.) Nkhani yokambirana. Yambani ndi kuonetsa vidiyo ya pa jw.org yakuti Musamangotengera Zochita za Anzanu (Pitani pamene palembedwa kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA.) Kenako funsani mafunso otsatirawa: Kodi ana amakumana ndi mavuto otani kusukulu? Kodi angagwiritse ntchito bwanji mfundo ya pa Ekisodo 23:2? Kodi ndi zinthu 4 ziti zimene zingawathandize kuti asamangotengera zochita za anzawo komanso kuti akhalebe okhulupirika kwa Mulungu? Pemphani achinyamata kuti afotokoze zinthu zabwino zimene anakumana nazo kusukulu.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: cl mutu 27 ndime 10-18 (30 min.)

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 149 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena