March Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano ya March 2016 Zitsanzo za Ulaliki March 7-13 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | ESITERE 6-10 Esitere Anasonyeza Kuti Sanali Wodzikonda KUWONJEZERA LUSO LATHU MU UTUMIKI Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki—Kukonza Ulaliki Wanuwanu wa Magazini MOYO WATHU WACHIKHRISTU Tidzalandire Bwino Alendo March 14-20 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOBU 1-5 Yobu Anakhalabe Wokhulupirika Pamene Ankayesedwa March 21-27 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOBU 6-10 Yobu Anasonyeza Kukhumudwa Kwake March 28–April 3 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOBU 11-15 Yobu Sankakayikira Kuti Akufa Adzauka MOYO WATHU WACHIKHRISTU Imfa ya Yesu Inathandiza Kuti Akufa Adzaukitsidwe