Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 March tsamba 6
  • March 28–April 3

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • March 28–April 3
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 March tsamba 6

March 28–April 3

YOBU 11-15

  • Nyimbo Na. 111 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yobu Sankakayikira Kuti Akufa Adzauka”: (10 min.)

    • Yobu 14:1, 2—Yobu ananena zinthu zimene zimasonyeza mmene moyo wa anthu ulili masiku ano (w15 3/1 3; w10 5/1 5 ndime 2; w08 3/1 3 ndime 3)

    • Yobu 14:13-15a—Yobu ankadziwa kuti Yehova sangamuiwale (w15 8/1 5; w14 1/1 7 ndime 4; w11 3/1 22 ndime 2-4)

    • Yobu 14:15b—Yehova amaona kuti atumiki ake okhulupirika ndi ofunika kwambiri (w15 8/1 7 ndime 3; w14 6/15 14 ndime 12; w11 3/1 22 ndime 3-6)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yobu 12:12—N’chifukwa chiyani tinganene kuti Akhristu achikulire angathandize Akhristu achinyamata? (g99 8/8 11, bokosi)

    • Yobu 15:27—Kodi Elifazi ankatanthauza chiyani pamene ananena kuti nkhope ya Yobu “yaphimbika ndi mafuta”? (it-1-E 802 ndime 4)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: Yobu 14:1-22 (Osapitirira 4 min.)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: fg phunziro 13, ndime 1—Muuzeni zimene mudzakambirane mukadzabweranso. (Osapitirira 2 min.)

  • Ulendo Wobwereza: fg phunziro 13, ndime 2—Kenako amuuze zimene adzaphunzire akadzabweranso. (Osapitirira 4 min.)

  • Phunziro la Baibulo: fg phunziro 13, ndime 3-4 (Osapitirira 6 min.)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 134

  • Zofunika pampingo: (5 min.)

  • “Imfa ya Yesu Inathandiza Kuti Akufa Adzaukitsidwe”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Pomaliza onetsani vidiyo imene inaonetsedwa pa Msonkhano Wachigawo wa 2014 wakuti, “Pitirizani Kufunafuna Ufumu wa Mulungu Choyamba.”

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: cl mutu 28 ndime 1-9 (30 min.)

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 33 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena