Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 March tsamba 5
  • March 21-27

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • March 21-27
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 March tsamba 5

March 21-27

YOBU 6-10

  • Nyimbo Na. 68 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yobu Anasonyeza Kukhumudwa Kwake”: (10 min.)

    • Yobu 6:1-3, 9, 10, 26; 7:11, 16—Munthu akakhumudwa amatha kuyankhula zinthu zimene sizili mumtima mwake (w13 8/15 19 ndime 7; w13 5/15 22 ndime 13)

    • Yobu 9:20-22—Yobu anaganiza molakwika kuti Mulungu analibe nazo ntchito ngakhale kuti iye anayesetsa kukhala wokhulupirika (w15 7/1 12 ndime 2)

    • Yobu 10:12—Ngakhale kuti anakumana ndi mavuto ambiri, Yobu ankanena zabwino za Yehova (w09 4/15 7 ndime 18; w09 4/15 10 ndime 13)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yobu 6:14​—Kodi Yobu anasonyeza bwanji kuti kukoma mtima kosatha n’kofunika? (w10 11/15 32 ndime 20)

    • Yobu 7:9, 10; 10:21—Ngati Yobu ankakhulupirira kuti akufa adzauka, n’chifukwa chiyani ananena zimene zili m’mavesiwa? (w06 3/15 14 ndime 11)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: Yobu 9:1-21 (Osapitirira 4 min.)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: wp16.2 16​—Muuzeni munthu amene mukumulalikirayo kuti angathe kupereka ndalama zothandizira ntchito yathu yapadziko lonse. (Osapitirira 2 min.)

  • Ulendo Wobwereza: wp16.2 16​—Muuzeni nkhani imene mudzaphunzire ulendo wotsatira. (Osapitirira 4 min.)

  • Phunziro la Baibulo: fg phunziro 2 ndime 6-8 (Osapitirira 6 min.)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 114

  • Muzichita Zinthu Mozindikira Mukamalimbikitsa Ena: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo imene akulu anaonera pa Sukulu ya Utumiki wa Ufumu yomwe inachitika posachedwapa. Kenako pemphani omvera kuti afotokoze mmene abale awiri a m’vidiyoyi asonyezera chitsanzo chabwino polimbikitsa munthu amene wakhumudwa chifukwa cha imfa ya munthu amene amam’konda.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: cl mutu 27 ndime 19-22 ndi bokosi patsamba 279 (30 min.)

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 27 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena