Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 November tsamba 8
  • November 28–December 4

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • November 28–December 4
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 November tsamba 8

November 28–December 4

NYIMBO YA SOLOMO 1-8

  • Nyimbo Na. 106 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Msulami Ndi Chitsanzo Chabwino Kwambiri kwa Atumiki a Yehova”: (10 min.)

    • [Onetsani vidiyo yakuti, Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Nyimbo ya Solomo.]

    • Nyimbo 2:7; 3:5—Msulami ankafunitsitsa kuti adikire mpaka atapeza munthu amene angamukonde ndi mtima wonse (w15 1/15 31 ndime 11-13)

    • Nyimbo 4:12; 8:8-10—Pa nthawi imene ankadikirayi anali wokhulupirika ndiponso wodzisunga (w15 1/15 32 ndime 14-16)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Nyimbo 2:1—Kodi Msulami anali ndi makhalidwe ati amene anamuchititsa kukhala wokongola kwambiri? (w15 1/15 31 ndime 13)

    • Nyimbo 8:6—N’chifukwa chiyani vesili limanena kuti chikondi chenicheni ndi “lawi la Ya”? (w15 1/15 29 ndime 3; w06 11/15 20 ndime 6)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Nyimbo 2:1-17

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) bhs—Gwiritsani ntchito vidiyo yakuti N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? kuti mugawire bukuli. (Dziwani izi: Musaonetse vidiyoyi m’chitsanzochi.)

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) bhs—Muitanireni munthuyo kumisonkhano.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 31-32 ndime 8-9

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 115

  • “Zimene Achinyamata Amadzifunsa—Kodi Ndafika Poti N’kukhala ndi Chibwenzi?”: (9 min.) Nkhani yochokera mu nkhani yakuti, “Zimene Achinyamata Amadzifunsa—Kodi Ndafika Poti N’kukhala ndi Chibwenzi?”

  • Kodi Ndi Chikondi Chenicheni Kapena Kungotengeka Maganizo?: (6 min.) Onetsani ndiponso kukambirana vidiyo yakuti Kodi Ndi Chikondi Chenicheni Kapena Kungotengeka Maganizo?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 12 ndime 1-12

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 34 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena