November Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano November 2016 Zitsanzo za Ulaliki November 7-13 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MIYAMBO 27-31 Baibulo Limafotokoza Zimene Mkazi Wabwino Amachita MOYO WATHU WACHIKHRISTU “Mwamuna Wake Amadziwika Pazipata” November 14-20 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MLALIKI 1-6 Muzisangalala Chifukwa Chogwira Ntchito Mwakhama MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kodi Tingagwiritse Ntchito Bwanji Buku Lakuti Zimene Baibulo Limaphunzitsa? November 21-27 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MLALIKI 7-12 “Kumbukira Mlengi Wako Wamkulu Masiku a Unyamata Wako” MOYO WATHU WACHIKHRISTU Achinyamata Musachedwe Kulowa ‘Pakhomo Lalikulu’ November 28–December 4 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | NYIMBO YA SOLOMO 1-8 Msulami Ndi Chitsanzo Chabwino Kwambiri kwa Atumiki a Yehova