Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 April tsamba 4
  • April 10-16

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • April 10-16
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 April tsamba 4

April 10-16

YEREMIYA 22-24

  • Nyimbo Na. 52 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Muli ndi ‘Mtima Wodziwa’ Yehova?”: (10 min.)

    • Yer. 24:1-3​—Yehova anayerekezera anthu ndi nkhuyu (w13 3/15 8 ¶2)

    • Yer. 24:4-7​—Nkhuyu zabwino zinkaimira anthu omwe anali ndi mtima womvera (w13 3/15 8 ¶4)

    • Yer. 24:8-10​—Nkhuyu zoipa zinkaimira anthu a mtima wopanduka ndi wosamvera (w13 3/15 8 ¶3)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yer. 22:30​—Kodi lamuloli likusonyeza kuti Yesu sanali woyenera kukhala pa mpando wachifumu wa Davide? (w07 3/15 10 ¶9)

    • Yer. 23:33​—Kodi “katundu wa Yehova” n’chiyani? (w07 3/15 11 ¶1)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yer 23:25-36

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) g17.2 tsamba loyamba​—Muuzeni nkhani imene mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) g17.2 tsamba loyamba​—Muuzeni nkhani imene mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) lv 5 ¶1-2​—Sonyezani mmene tingafikire pamtima wophunzira wathu.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 60

  • “Mungathe Kulimbikitsa Mkhristu Amene Anafooka”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo yakuti Muzilimbikitsa Amene Anafooka.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 21 ¶13-22, komanso Mfundo Zofunika Kuziganizira patsamba 186

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 93 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena