Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 August tsamba 3
  • Yehova Anapereka Cholowa kwa Anthu Omwe Sankamulambira

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yehova Anapereka Cholowa kwa Anthu Omwe Sankamulambira
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Nkhani Yofanana
  • Yehova Amapereka Mphoto kwa Anthu Omufunafuna ndi Mtima Wonse
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2016
  • Ulosi Wonena za Kuwonongedwa kwa Turo Umatithandiza Kuti Tizikhulupirira Kwambiri Mawu a Yehova
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Kodi Mukudziwa?
    Nsanja ya Olonda—2008
  • Kupereka Nsembe Zokondweretsa Mulungu
    Nsanja ya Olonda—2007
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 August tsamba 3

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EZEKIELI 28-31

Yehova Anapereka Cholowa kwa Anthu Omwe Sankamulambira

29:18-20

Ngati Yehova anapereka mphoto kwa anthu omwe sankamulambira chifukwa cha ntchito imene anagwira, ndiye kuli bwanji kwa atumiki ake okhulupirika?

ZIMENE ABABULO ANACHITA

Anagonjetsa mzinda wa Turo

Asilikali a Babulo azinga mzinda wa Turo

ZIMENE INEYO NDIKUCHITA

Kodi ndikuchita zotani pankhondo yanga yauzimu?

MMENE ABABULO ANADZIPEREKERA

  • Kudzipereka kwa Ababulo kukuphatikizapo zimene anachita pozinga mzinda wa Turo kwa zaka 13

    Anazinga mzinda wa Turo kwa zaka 13

  • Kudzipereka kwa Ababulo kunaphatikizapo kuti asilikali ake ankasowa zinthu zina pamoyo wawo

    Asilikali a Babulo ankasowa zinthu zina pamoyo wawo

  • Kudzipereka kwa Ababulo kunaphatikizapo kuti sanapatsidwe malipiro aliwonse

    Ababulo sanapatsidwe malipiro aliwonse

MMENE NDIKUDZIPEREKERA

Kodi ndimachita zotani potumikira Yehova?

KODI YEHOVA ANAWAPATSA CHIYANI ABABULO?

Yehova anawapatsa dziko la Iguputo kuti alande chuma chake

Bokosi la zinthu zamtengo wapatali

MADALITSO AMENE YEHOVA WANDIPATSA

Kodi Yehova wandipatsa madalitso otani?

Gwirizanitsani mavesiwa ndi mawu ali m’munsiwa.

  • Rute 2:12

  • Mal. 3:16

  • Aheb. 6:10

  • “Pakuti Mulungu si wosalungama woti angaiwale ntchito yanu ndi chikondi chimene munachisonyeza pa dzina lake.”

  • “Yehova akudalitse chifukwa cha zimene wachita, ndipo Yehova, Mulungu wa Isiraeli akufupe mokwanira.”

  • “Buku la chikumbutso linayamba kulembedwa pamaso pake. Buku limeneli linali lonena za anthu oopa Yehova ndi anthu amene anali kuganizira za dzina lake.”

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena