Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 March tsamba 3
  • March 12-18

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • March 12-18
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 March tsamba 3

March 12-18

Mateyu 22-23

  • Nyimbo Na. 30 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muzitsatira Malamulo Awiri Aakulu Kwambiri”: (10 min.)

    • Mat. 22:36-38​—Kodi mavesi amenewa akusonyeza kuti kumvera lamulo lalikulu kwambiri m’Chilamulo kumaphatikizapo chiyani? (Mfundo zimene ndikuphunzira za “mtima,” “moyo,” “maganizo” pa Mat. 22:37, nwtsty)

    • Mat. 22:39​—Kodi lamulo lalikulu lachiwiri ndi liti? (Mfundo zimene ndikuphunzira za “Lachiwiri,” “mnzako” pa Mat. 22:39, nwtsty)

    • Mat. 22:40​—Mfundo za m’Malemba Achiheberi zagona pa chikondi (Mfundo zimene ndikuphunzira za “Chilamulo . . . Zolemba za Aneneri,” “chagona” pa Mat. 22:40, nwtsty)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Mat. 22:21​—Kodi “zinthu za Kaisara” ndi ziti, nanga “za Mulungu” ndi ziti? (Mfundo zimene ndikuphunzira za “zinthu za Kaisara kwa Kaisara,” “za Mulungu” pa Mat. 22:21, nwtsty)

    • Mat. 23:24​—Kodi mawu a Yesu amenewa akutanthauza chiyani? (Mfundo zimene ndikuphunzira za “amene mumasefa zakumwa zanu kuti muchotsemo kanyerere koma mumameza ngamila” pa Mat. 23:24, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mat. 22:1-22

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene.

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 199 ¶8-9​—Limbikitsani wophunzira Baibulo wanu kuti aitanire anzake ku mwambo wa Chikumbutso.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 96

  • “Kodi Tingasonyeze Bwanji Kuti Timakonda Mulungu Komanso Anzathu?” (15 min.) Nkhani yokambirana. Pofuna kusonyeza kufunika koganizira komanso kuona m’maganizo mwathu zimene tikuwerenga m’Baibulo, mvetserani mbali ya sewero la mawu okha lakuti, Yehova Yekha Ndiye Mulungu Woona. Ndipo onse azitsatira m’Mabaibulo awo pa 1 Mafumu 18:17-46.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 15 ¶9-17

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 52 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena