March Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya March 2018 Zimene Tinganene March 5-11 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MATEYU 20-21 “Aliyense Wofuna Kukhala Wamkulu Pakati Panu Ayenera Kukhala Mtumiki Wanu” March 12-18 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MATEYU 22-23 Muzitsatira Malamulo Awiri Aakulu Kwambiri MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kodi Tingasonyeze Bwanji Kuti Timakonda Mulungu Komanso Anzathu? March 19-25 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MATEYU 24 Pitirizani Kukhala Maso M’masiku Otsiriza Ano MOYO WATHU WACHIKHRISTU Mapeto a Dziko Loipali Ali Pafupi Kwambiri March 26–April 1 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MATEYU 25 “Khalanibe Maso” MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki—Muzithandiza Ophunzira Anu Kuti Azikonzekera