CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Kodi Mungatsanzire Bwanji Anaziri?
Anaziri ankalolera kudzimana zinthu zina (Nu 6:2-4; it-2 477)
Anaziri ankagonjera n’kumatsatira zofuna za Yehova (Nu 6:5)
Anaziri ankachita zonse zimene Yehova ankafuna kuti akhalebe oyera (Nu 6:6, 7)
Masiku ano, Akhristu amene ali muutumiki wa nthawi zonse amasonyeza mtima wodzimana ndipo amagonjera Yehova komanso dongosolo lake.