January Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu January-February 2021 January 4-10 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Pitirizani Kukhala Ndi Makhalidwe Oyera MOYO WATHU WACHIKHRISTU Makolo Muzithandiza Ana Anu Kukhala Odziwa Zinthu January 11-17 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Yehova Amafuna Kuti Anthu Ake Azikhala Osiyana ndi Ena MOYO WATHU WACHIKHRISTU Tetezani Banja Lanu January 18-24 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Zikondwerero Zomwe Zimatikhudza MOYO WATHU WACHIKHRISTU Misonkhano Yachigawo Imatipatsa Mwayi Wosonyezana Chikondi January 25-31 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Chaka cha Ufulu Komanso Ufulu Womwe Tidzakhale Nawo M’tsogolo MOYO WATHU WACHIKHRISTU Timathokoza Mulungu ndi Khristu Chifukwa cha Ufulu Womwe Tidzakhale Nawo February 1-7 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kodi Mungatani Kuti Yehova Azikudalitsani? MOYO WATHU WACHIKHRISTU Sankhani Kutumikira Yehova February 8-14 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Yehova Amachita Zinthu Mwadongosolo Ndi Anthu Ake MOYO WATHU WACHIKHRISTU N’zotheka Kulalikira kwa Aliyense February 15-21 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Utumiki wa Alevi February 22-28 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kodi Mungatsanzire Bwanji Anaziri? MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kodi Mudzachita Upainiya Wothandiza M’mwezi wa March Kapena April? KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI Zimene Tinganene