Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 September tsamba 12
  • Muzitumikira Yehova Ndi Mtima Wonse

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muzitumikira Yehova Ndi Mtima Wonse
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Mumatsatira Yehova ndi Mtima Wonse?
    Nsanja ya Olonda—1993
  • Anthu 12 Anapita Kukaona Dziko la Kanani
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Zimene Ndikuphunzira M’Baibulo
    Nsanja ya Olonda—2012
  • Khulupirirani Yehova ndi Mtima Wanu Wonse
    Nsanja ya Olonda—2003
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 September tsamba 12

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muzitumikira Yehova Ndi Mtima Wonse

Kalebe anayamba kutumikira Yehova ali wachinyamata (Yos 14:7, 8)

Patapita nthawi, Kalebe anadalira Yehova kuti akwanitse utumiki wovuta womwe anamupatsa (Yos 14:10-12; w04 12/1 11 ¶11)

Kalebe analandira madalitso chifukwa chotumikira Yehova ndi mtima wonse (Yos 14:13, 14; w06 10/1 18 ¶11)

Zithunzi: Chithunzi cha mlongo wokhulupirika amene akupirira mavuto obwera chifukwa cha uchikulire. 1. Wakhala pansi atagwira ndodo ndipo akupemphera. 2. Akulalikira pa malo opezeka anthu ambiri ali ndi mlongo wachitsikana. 3. Akuonetsa zithunzi ana akumpingo kwawo. 4. Akumwetulira.

Chikhulupiriro cha Kalebe chinalimba chifukwa chotsatira malangizo a Yehova komanso kuona madalitso amene ankalandira. Ifenso tikamaona Yehova akuyankha mapemphero athu komanso kutitsogolera m’njira zosiyanasiyana zimatilimbikitsa kupitirizabe kum’tumikira.​—1Yo 5:14, 15.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena