November 1-7
YOSWA 18-19
Nyimbo Na. 12 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yehova Anachita Zinthu Mwanzeru Pogawa Malo”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Yos 18:1-3—Kodi n’kutheka kuti n’chiyani chomwe chinachititsa Aisiraeli kuzengereza kukalanda dera lomwe linali kumadzulo kwa Yorodano? (it-1 359 ¶5)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yos 18:1-14 (th phunziro 2)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Uthenga Wabwino—Sl 37:10, 11. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.
Ulendo Woyamba: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako mugawireni Nsanja ya Olonda Na. 2 2021. (th phunziro 1)
Ulendo Woyamba: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 11)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Timathokoza Yehova Chifukwa cha Chikondi Chanu”: (15 min.) Nkhani yokambirana yokambidwa ndi mkulu. Onerani vidiyo yakuti Nthawi Zonse ‘Timayamika Mulungu Chifukwa cha Inu.’ Tchulani mfundo imodzi kapena ziwiri za munkhani zakuti “Kodi Zopereka Zanu Zimagwiritsidwa Ntchito Bwanji?” zopezeka pa jw.org.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 7 ndime 1-9, mawu akumapeto 19, 20
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 141 ndi Pemphero