Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 November tsamba 2
  • Yehova Anachita Zinthu Mwanzeru Pogawa Malo

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yehova Anachita Zinthu Mwanzeru Pogawa Malo
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Yehova Anamenyera Nkhondo Aisiraeli
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Muziteteza Cholowa Chanu Chomwe Ndi Chamtengo Wapatali
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Mawu Omaliza Amene Yoswa Analimbikitsa Nawo Mtundu wa Aisiraeli
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Yehova Amafuna Kuti Anthu Ake Azikhala Osiyana ndi Ena
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 November tsamba 2
Zithunzi: 1. Yakobo atatsala pang’ono kumwalira akulosera zokhudza ana ake. 2. Mapu a Dziko Lolonjezedwa osonyeza mmene malo anagawidwira kwa mafuko 12 a Isiraeli.

Yakobo akulosera zokhudza ana ake

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Anachita Zinthu Mwanzeru Pogawa Malo

Yehova anagawa malo pogwiritsa ntchito maere, mwina pofuna kupereka malo enieni amene fuko lililonse linkafunika kulandira (Yos 18:10; it-1 359 ¶1)

Yehova anaonetsetsa kuti ulosi umene Yakobo ananena atatsala pang’ono kumwalira wakwaniritsidwa (Yos 19:1; it-1 1200 ¶1)

Yehova analola kuti anthu azigawana okha kukula kwa malo amene fuko lililonse lingapatsidwe (Yos 19:9; it-1 359 ¶2)

Malowa anagawidwa m’njira yakuti mafuko asamakangane kapena kuchitirana nsanje. Kodi zimenezi zikukutsimikizirani kuti Yehova adzachita zinthu motani m’dziko latsopano?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena