APRIL 6-12
YESAYA 50-51
Nyimbo Na. 88 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)
1. Muzimvera Yesu Yemwe Anaphunzitsidwa ndi Yehova
(10 min.)
Yesu anaphunzitsidwa ndi Yehova asanabwere padziko lapansi (Yes 50:4; kr 182 ¶5-mwbr)
Yesu ankafunitsitsa kuphunzira (Yes 50:5; cf 133 ¶13-mwbr)
Anthu amene amaopa Yehova amamvera mawu a Mtumiki wake Yesu (Yes 50:10; Yoh 10:27)
FUNSO LOFUNIKA KULIGANIZIRA: Kodi tingatsanzire bwanji Yesu pa nkhani yokhala wofunitsitsa kuphunzitsidwa ndi Yehova?—1Pet 2:21.
2. Mfundo Zothandiza
(10 min.)
Yes 51:1—Kodi vesili likutanthauza chiyani? (it-E “Malo Okumbapo Miyala” ¶2-mwbr)
Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
3. Kuwerenga Baibulo
(4 min.) Yes 50:1-11 (th phunziro 2)
4. Ulendo Woyamba
(3 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Fotokozerani mnzanu wakuntchito zokhudza Chikumbutso. (lmd phunziro 2, mfundo 4)
5. Ulendo Wobwereza
(4 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. Itanirani mwininyumba yemwe anapezeka ku Chikumbutso kumisonkhano yotsatira. (lmd phunziro 9, mfundo 4)
6. Kufotokoza Zimene Mumakhulupirira
(5 min.) Chitsanzo. ijwbq nkhani na. 140 ¶4—Mutu: Kodi Kungokhulupirira Yesu N’kokwanira Kuti Tidzapulumuke? (lmd phunziro 11, mfundo 5)
Nyimbo Na. 99
7. Zofunika Pampingo
(15 min.)
8. Phunziro la Baibulo la Mpingo
(30 min.) ) lfb mawu oyamba a gawo 12 komanso mutu 74-75