Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • ijwbq nkhani 2
  • Kodi Nkhani za M’Baibulo Ndi Maganizo a Mulungu?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Nkhani za M’Baibulo Ndi Maganizo a Mulungu?
  • Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • Yankho la m’Baibulo
  • Kodi Dzina la Buku la M’Baibulo, Lakuti Chivumbulutso, Limatanthauza Chiyani?
    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
  • Kodi Mudzanena Kuti,“Ndine Pano! Munditumize Ine”?
    Nsanja ya Olonda—1987
  • Mmene Masomphenya a M’buku la Chivumbulutso Akukukhudzirani
    Mapeto Osangalatsa a Masomphenya a M’buku la Chivumbulutso
  • Aisiraeli Anapempha Kuti Akhale ndi Mfumu
    Kodi Baibulo Lili Ndi Uthenga Wotani?
Onani Zambiri
Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
ijwbq nkhani 2
Munthu akulemba mumpukutu

Kodi Nkhani za M’Baibulo Ndi Maganizo a Mulungu?

Yankho la m’Baibulo

Anthu ambiri amene analemba Baibulo amanena kuti Mulungu ndi amene anawauza zimene analembazo. Taonani zitsanzo izi:

  • Mfumu Davide inati: “Mzimu wa Yehova unandilankhulitsa, ndipo mawu ake anali palilime langa.”—2 Samueli 23:1, 2.

  • Mneneri Yesaya anati: “[Izi ndi zimene] Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena.”—Yesaya 22:15.

  • Mtumwi Yohane anati: “Chivumbulutso choperekedwa ndi Yesu Khristu, chimene Mulungu anamupatsa.”—Chivumbulutso 1:1.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena