Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • ijwbq nkhani 3
  • Kodi Baibulo Ndi Buku la Azungu?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Baibulo Ndi Buku la Azungu?
  • Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • Yankho la m’Baibulo
  • Yehova “Alibe Tsankho”
    Nsanja ya Olonda—2013
  • Kodi Mulungu Amaona Kuti Mtundu Wina Wa Anthu Ndi Wofunika Kuposa Mitundu Ina?
    Nsanja ya Olonda—2011
  • Kodi Mulungu Angayankhe Mapemphero Anga?
    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
  • Kodi Baibulo Limanena Zotani?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2017
Onani Zambiri
Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
ijwbq nkhani 3
Munthu akuphunzira Baibulo

Kodi Baibulo Ndi Buku la Azungu?

Yankho la m’Baibulo

Baibulo silinalembedwe ndi azungu. Anthu onse amene Mulungu anawagwiritsira ntchito polemba Baibulo anali a ku Asia. Ndipotu, Baibulo silisonyeza kuti mtundu wina wa anthu ndi wapamwamba kuposa mtundu wina. Baibulo limanena kuti: “Mulungu alibe tsankho. Iye amalandira munthu wochokera mu mtundu uliwonse, amene amamuopa ndi kuchita chilungamo.”—Machitidwe 10:34, 35.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena