EKISODO
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
Aisiraeli anachulukana ku Iguputo (1-7)
Farao anazunza Aisiraeli (8-14)
Azamba oopa Mulungu anapulumutsa ana (15-22)
2
Kubadwa kwa Mose (1-4)
Mwana wamkazi wa Farao anatenga Mose kuti akhale mwana wake (5-10)
Mose anathawira ku Midiyani ndipo anakwatira Zipora (11-22)
Mulungu anamva kulira kwa Aisiraeli (23-25)
3
Mose komanso chitsamba chaminga choyaka moto (1-12)
Yehova anafotokoza za dzina lake (13-15)
Yehova anapatsa Mose malangizo (16-22)
4
Zizindikiro zitatu zimene Mose anachita (1-9)
Mose ankadziona kuti sangakwanitse ntchito imene Mulungu anamupatsa (10-17)
Mose anabwerera ku Iguputo (18-26)
Mose anakumananso ndi Aroni (27-31)
5
Mose ndi Aroni anapita kwa Farao (1-5)
Aisiraeli anapitiriza kuzunzidwa kwambiri (6-18)
Aisiraeli anayamba kuimba mlandu Mose komanso Aroni (19-23)
6
Anawauzanso lonjezo lakuti adzawalanditsa ku ukapolo (1-13)
Mzere wobadwira wa Mose ndi Aroni (14-27)
Mose anakaonekeranso pamaso pa Farao (28-30)
7
Yehova analimbikitsa Mose (1-7)
Ndodo ya Aroni inasanduka njoka yaikulu (8-13)
Mliri woyamba: madzi anasanduka magazi (14-25)
8
Mliri wachiwiri: achule (1-15)
Mliri wachitatu: tizilombo touluka toyamwa magazi (16-19)
Mliri wa 4: ntchentche zoluma (20-32)
9
Mliri wa 5: kufa kwa ziweto (1-7)
Mliri wa 6: zithupsa pa anthu ndi nyama (8-12)
Mliri wa 7: mvula ya matalala (13-35)
10
11
12
Kukhazikitsidwa kwa Pasika (1-28)
Mliri wa 10: ana oyamba kubadwa anaphedwa (29-32)
Aisiraeli anachoka ku Iguputo (33-42)
Malangizo okhudza kuchita nawo Pasika (43-51)
13
Mwana wamwamuna woyamba kubadwa aliyense ndi wa Yehova (1, 2)
Chikondwerero cha Mikate Yopanda Zofufumitsa (3-10)
Mwana wamwamuna woyamba kubadwa aliyense ankaperekedwa kwa Mulungu (11-16)
Aisiraeli anatsogoleredwa kupita ku Nyanja Yofiira (17-20)
Chipilala cha mtambo komanso cha moto (21, 22)
14
Aisiraeli anafika panyanja (1-4)
Farao analondola Aisiraeli (5-14)
Aisiraeli anaoloka Nyanja Yofiira (15-25)
Aiguputo anamira mʼnyanja (26-28)
Aisiraeli anakhulupirira Yehova (29-31)
15
Mose ndi Aisiraeli anaimba nyimbo yosonyeza kupambana (1-19)
Miriamu anathirira mangʼombe (20, 21)
Madzi owawa anakhala okoma (22-27)
16
Anthu anangʼungʼudza zokhudza chakudya (1-3)
Yehova anamva kungʼungʼudza kwa anthu (4-12)
Anapatsidwa zinziri ndi mana (13-21)
Mana sankapezeka tsiku la Sabata (22-30)
Anasunga mana kuti chikhale chikumbutso (31-36)
17
Anadandaula za kusowa kwa madzi ku Horebu (1-4)
Madzi anatuluka kuchokera mʼthanthwe (5-7)
Aamaleki anakaukira Aisiraeli koma anagonjetsedwa (8-16)
18
19
Paphiri la Sinai (1-25)
Isiraeli adzakhala ufumu wa ansembe (5, 6)
Anthu anayeretsedwa kuti akumane ndi Mulungu (14, 15)
20
21
22
23
Zigamulo zoti Aisiraeli azitsatira (1-19)
Mngelo anatsogolera Aisiraeli (20-26)
Kutenga dziko komanso malire ake (27-33)
24
25
26
27
28
Zovala za ansembe (1-5)
Efodi (6-14)
Chovala pachifuwa (15-30)
Malaya odula manja (31-35)
Nduwira ndi kachitsulo kagolide (36-39)
Zovala zina za ansembe (40-43)
29
30
Guwa la nsembe zofukiza (1-10)
Kalembera komanso ndalama zophimbira machimo (11-16)
Beseni losambira lakopa (17-21)
Mafuta odzozera osakanizidwa mwapadera (22-33)
Kapangidwe ka zofukiza zopatulika (34-38)
31
32
33
Uthenga wa Mulungu wowadzudzula (1-6)
Chihema chokumanako kunja kwa msasa (7-11)
Mose anapempha kuti aone ulemerero wa Yehova (12-23)
34
Anapanganso miyala ina yosema (1-4)
Mose anaona ulemerero wa Yehova (5-9)
Mfundo zokhudza pangano zinabwerezedwa (10-28)
Nkhope ya Mose inkawala (29-35)
35
Malangizo okhudza Sabata (1-3)
Zopereka za chihema (4-29)
Bezaleli komanso Oholiabu anapatsidwa mzimu wa Mulungu (30-35)
36
37
38
39
Kupanga zovala za ansembe (1)
Efodi (2-7)
Chovala pachifuwa (8-21)
Malaya odula manja (22-26)
Zovala zina za ansembe (27-29)
Kachitsulo kagolide (30, 31)
Mose anayendera chihema (32-43)
40