1 SAMUELI
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
Elikana ndi akazi ake (1-8)
Hana anapemphera kuti akhale ndi mwana (9-18)
Samueli anabadwa nʼkuperekedwa kwa Yehova (19-28)
2
3
4
5
6
7
Likasa ku Kiriyati-yearimu (1)
Samueli anati: ‘Muzitumikira Yehova yekha’ (2-6)
Aisiraeli anapambana ku Mizipa (7-14)
Samueli anayamba kuweruza Aisiraeli (15-17)
8
Aisiraeli anati akufuna mfumu (1-9)
Samueli anachenjeza anthu (10-18)
Yehova anawapatsa mfumu (19-22)
9
10
11
12
13
Sauli anasankha asilikali (1-4)
Sauli anachita zinthu modzikuza (5-9)
Samueli anadzudzula Sauli (10-14)
Aisiraeli analibe zida (15-23)
14
Zimene Yonatani anachita ku Mikimasi (1-14)
Mulungu anagonjetsa adani a Aisiraeli (15-23)
Sauli analumbira mopupuluma (24-46)
Nkhondo za Sauli; banja lake (47-52)
15
Sauli sanamvere ndipo sanaphe Agagi (1-9)
Samueli anadzudzula Sauli (10-23)
Sauli anakanidwa kuti asakhalenso mfumu (24-29)
Samueli anapha Agagi (30-35)
16
Samueli anadzoza Davide kukhala mfumu yotsatira (1-13)
Mzimu wa Mulungu unamuchokera Sauli (14-17)
Davide ankaimbira Sauli zeze (18-23)
17
18
Ubwenzi wa Davide ndi Yonatani (1-4)
Sauli anayamba kuchitira nsanje Davide (5-9)
Sauli ankafuna kupha Davide (10-19)
Davide anakwatira Mikala mwana wa Sauli (20-30)
19
20
21
22
Davide ku Adulamu ndi ku Mizipe (1-5)
Sauli anapha ansembe a ku Nobu (6-19)
Abiyatara anapulumuka (20-23)
23
Davide anapulumutsa mzinda wa Keila (1-12)
Sauli ankasakasaka Davide (13-15)
Yonatani analimbikitsa Davide (16-18)
Sauli anangotsala pangʼono kupeza Davide (19-29)
24
25
Samueli anamwalira (1)
Nabala anakana kuthandiza anyamata a Davide (2-13)
Abigayeli anachita zinthu mwanzeru (14-35)
Yehova anapha Nabala wopanda nzeru (36-38)
Abigayeli anakhala mkazi wa Davide (39-44)
26
27
28
29
30
31