ESITERE
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
Phwando la Mfumu Ahasiwero ku Susani (1-9)
Mfumukazi Vasiti anakana kumvera mfumu (10-12)
Mfumu inafunsira malangizo kwa amuna anzeru (13-20)
Mfumu inatumiza makalata (21, 22)
2
Kufufuza mfumukazi yatsopano (1-14)
Esitere anakhala mfumukazi (15-20)
Moredikayi anaulula chiwembu (21-23)
3
4
5
6
7
8
Moredikayi anakwezedwa (1, 2)
Esitere anachonderera mfumu (3-6)
Lamulo la mfumu loti Ayuda adziteteze (7-14)
Ayuda anapeza mtendere ndipo anayamba kusangalala (15-17)
9
10