MACHITIDWE
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
Mawu oyamba opita kwa Teofilo (1-5)
Kulalikira mpaka kumalekezero a dziko lapansi (6-8)
Yesu anapita kumwamba (9-11)
Ophunzira anasonkhana mogwirizana (12-14)
Matiya anasankhidwa kuti alowe mʼmalo mwa Yudasi (15-26)
2
Anthu analandira mzimu woyera pa Pentekosite (1-13)
Nkhani imene Petulo anakamba (14-36)
Anthu anatsatira zimene Petulo ananena (37-41)
Akhristu ankachitira zinthu limodzi (42-47)
3
4
Petulo ndi Yohane anamangidwa (1-4)
Kuweruzidwa ndi Khoti Lalikulu la Ayuda (5-22)
Anapemphera kuti akhale olimba mtima (23-31)
Ophunzira ankagawana zinthu (32-37)
5
Hananiya ndi Safira (1-11)
Atumwi anachita zizindikiro zambiri (12-16)
Anamangidwa nʼkumasulidwa (17-21a)
Anapita nawonso ku Khoti Lalikulu la Ayuda (21b-32)
Malangizo a Gamaliyeli (33-40)
Kulalikira kunyumba ndi nyumba (41, 42)
6
7
8
Saulo ankazunza anthu (1-3)
Utumiki wa Filipo unkayenda bwino ku Samariya (4-13)
Petulo ndi Yohane anatumizidwa ku Samariya (14-17)
Simoni ankafuna kugula mzimu woyera (18-25)
Nduna ya ku Itiyopiya (26-40)
9
Saulo ali pa ulendo wa ku Damasiko (1-9)
Hananiya anatumizidwa kuti akathandize Saulo (10-19a)
Saulo analalikira za Yesu ku Damasiko (19b-25)
Saulo anapita ku Yerusalemu (26-31)
Petulo anachiritsa Eneya (32-35)
Dolika, yemwe anali wopatsa, anaukitsidwa (36-43)
10
Masomphenya a Koneliyo (1-8)
Masomphenya a Petulo a nyama zoyeretsedwa (9-16)
Petulo anapita kunyumba kwa Koneliyo (17-33)
Petulo analalikira uthenga wabwino kwa anthu a mitundu ina (34-43)
Anthu a mitundu ina analandira mzimu woyera nʼkubatizidwa (44-48)
11
Petulo anakapereka lipoti kwa atumwi (1-18)
Baranaba ndi Saulo anapita ku Antiokeya wa ku Siriya (19-26)
Agabo analosera za njala (27-30)
12
Yakobo anaphedwa; Petulo anamangidwa (1-5)
Petulo anamasulidwa modabwitsa (6-19)
Herode anaphedwa ndi mngelo (20-25)
13
Baranaba ndi Saulo anatumizidwa kuti akakhale amishonale (1-3)
Utumiki wa ku Kupuro (4-12)
Zimene Paulo analankhula ku Antiokeya wa ku Pisidiya (13-41)
Ulosi woti ayambe kulalikira kwa anthu a mitundu ina (42-52)
14
Okhulupirira anawonjezeka ku Ikoniyo; anayamba kutsutsidwa (1-7)
Ankawayesa kuti ndi milungu ku Lusitara (8-18)
Paulo anapulumuka atamuponya miyala (19, 20)
Analimbikitsa mipingo (21-23)
Anabwerera ku Antiokeya wa ku Siriya (24-28)
15
Anatsutsana ku Antiokeya pa nkhani ya mdulidwe (1, 2)
Nkhaniyi anapita nayo ku Yerusalemu (3-5)
Akulu ndi atumwi anakumana kuti akambirane (6-21)
Kalata yochokera ku bungwe lolamulira (22-29)
Mipingo inalimbikitsidwa ndi kalata (30-35)
Paulo ndi Baranaba anasiyana (36-41)
16
Paulo anasankha Timoteyo (1-5)
Masomphenya a munthu wa ku Makedoniya (6-10)
Lidiya anakhala Mkhristu ku Filipi (11-15)
Paulo ndi Sila anamangidwa (16-24)
Woyangʼanira ndende ndi banja lake anabatizidwa (25-34)
Paulo ananena kuti akuluakulu a zamalamulo apepese (35-40)
17
Paulo ndi Sila ku Tesalonika (1-9)
Paulo ndi Sila ku Bereya (10-15)
Paulo ku Atene (16-22a)
Zimene Paulo analankhula kubwalo la Areopagi (22b-34)
18
Utumiki wa Paulo ku Korinto (1-17)
Anabwerera ku Antiokeya wa ku Siriya (18-22)
Paulo anachoka ku Galatiya ndi ku Fulugiya (23)
Apolo, yemwe ankalankhula mwaluso, anathandizidwa (24-28)
19
Paulo ku Efeso; anthu ena anabatizidwanso (1-7)
Ntchito yolalikira ya Paulo (8-10)
Utumiki unkayenda bwino ngakhale kuti ena ankakhulupirira zamizimu (11-20)
Chisokonezo ku Efeso (21-41)
20
Paulo ku Makedoniya ndi ku Girisi (1-6)
Utiko anaukitsidwa ku Torowa (7-12)
Kuchoka ku Torowa kupita ku Mileto (13-16)
Paulo anakumana ndi akulu a ku Efeso (17-38)
21
Ulendo wa ku Yerusalemu (1-14)
Anafika ku Yerusalemu (15-19)
Paulo anatsatira malangizo a akulu (20-26)
Chisokonezo mʼkachisi; Paulo anamangidwa (27-36)
Paulo analoledwa kulankhula ndi gulu la anthu (37-40)
22
Mawu a Paulo odziteteza pamaso pa gulu la anthu (1-21)
Paulo anagwiritsa ntchito mwayi wokhala nzika ya Roma (22-29)
Khoti Lalikulu la Ayuda linakumana (30)
23
Paulo analankhula pamaso pa Khoti Lalikulu la Ayuda (1-10)
Paulo analimbikitsidwa ndi Ambuye (11)
Chiwembu chofuna kupha Paulo (12-22)
Paulo anapititsidwa ku Kaisareya (23-35)
24
Milandu imene Paulo ankaimbidwa (1-9)
Paulo anadziteteza pamaso pa Felike (10-21)
Mlandu wa Paulo unaimitsidwa kwa zaka ziwiri (22-27)
25
Mlandu wa Paulo pamaso pa Fesito (1-12)
Fesito anafunsa nzeru kwa Mfumu Agiripa (13-22)
Paulo anaonekera kwa Agiripa (23-27)
26
Paulo anadziteteza pamaso pa Agiripa (1-11)
Paulo anafotokoza mmene anakhalira Mkhristu (12-23)
Zimene Fesito ndi Agiripa anachita (24-32)
27
28
Anafika kugombe la ku Melita (1-6)
Bambo ake a Papuliyo anachiritsidwa (7-10)
Ulendo wa ku Roma (11-16)
Paulo analankhula ndi Ayuda ku Roma (17-29)
Paulo analalikira molimba mtima kwa zaka ziwiri (30, 31)