AKOLOSE
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
Moni (1, 2)
Kuthokoza chifukwa cha chikhulupiriro cha Akolose (3-8)
Kuwapempherera kuti akule mwauzimu (9-12)
Udindo waukulu wa Khristu (13-23)
Paulo anagwira ntchito mwakhama pothandiza mpingo (24-29)
2
Chinsinsi chopatulika cha Mulungu, Khristu (1-5)
Samalani ndi anthu opusitsa anzawo (6-15)
Zenizeni zake zinakwaniritsidwa ndi Khristu (16-23)
3
4
Malangizo opita kwa ambuye (1)
“Muzilimbikira kupemphera” (2-4)
Kuchita zinthu mwanzeru pokhala ndi anthu akunja (5, 6)
Moni womaliza (7-18)