1 ATESALONIKA
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
2
Utumiki wa Paulo ku Tesalonika (1-12)
Atesalonika analandira mawu a Mulungu (13-16)
Paulo ankalakalaka kuona Atesalonika (17-20)
3
Paulo anapitiriza kukhala ku Atene podikira lipoti lochokera ku Tesalonika (1-5)
Timoteyo anabweretsa lipoti lolimbikitsa (6-10)
Anapempherera Atesalonika (11-13)
4
Anawachenjeza kuti azipewa chiwerewere (1-8)
Muzikondana kwambiri kuposa mmene mukuchitira (9-12)
Amene anafa mwa Khristu adzakhala oyambirira kuuka (13-18)
5