2 TIMOTEYO
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
Moni (1, 2)
Paulo anayamikira Mulungu chifukwa cha chikhulupiriro cha Timoteyo (3-5)
Kukolezera moto mphatso yochokera kwa Mulungu (6-11)
Gwiritsitsabe mawu olondola (12-14)
Adani ndi anzake a Paulo (15-18)
2
Kuphunzitsa oyenerera kukhala aphunzitsi (1-7)
Kuvutika chifukwa cha uthenga wabwino (8-13)
Kufotokoza bwino mawu a choonadi (14-19)
Kuthawa zilakolako za unyamata (20-22)
Zoyenera kuchita ndi otsutsa (23-26)
3
Masiku otsiriza adzakhala nthawi yovuta (1-7)
Kutsatira chitsanzo cha Paulo (8-13)
“Pitiriza kutsatira zimene unaphunzira” (14-17)
4
“Uzikwaniritsa mbali zonse za utumiki wako” (1-5)
“Ndamenya nkhondo yabwino” (6-8)
Zina zomwe Paulo ananena (9-18)
Kupereka moni (19-22)