2 PETULO
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
2
Kudzakhala aphunzitsi abodza (1-3)
Umboni wotsimikizira kuti aphunzitsi abodza adzaweruzidwa (4-10a)
Mmene tingadziwire aphunzitsi abodza (10b-22)
3
Anthu onyoza amakayikira zoti anthu oipa adzawonongedwa (1-7)
Yehova sakuchedwa (8-10)
Ganizirani za mtundu wa anthu amene muyenera kukhala (11-16)
Chenjerani kuti anthu asakusocheretseni (17, 18)