1 TIMOTEYO
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
Moni (1, 2)
Chenjezo lokhudza aphunzitsi abodza (3-11)
Paulo anasonyezedwa kukoma mtima kwakukulu (12-16)
Mfumu yamuyaya (17)
“Kumenya nkhondo yabwino” (18-20)
2
3
Zoyenera kuti munthu akhale woyangʼanira (1-7)
Zoyenera kuti munthu akhale mtumiki wothandiza (8-13)
Chinsinsi chopatulika cha kudzipereka kwa Mulungu (14-16)
4
Chenjezo lokhudza zomwe ziwanda zimaphunzitsa (1-5)
Kukhala mtumiki wabwino wa Khristu (6-10)
Uzisamala ndi zimene umaphunzitsa (11-16)
5
Zoyenera kuchita ndi achikulire komanso achinyamata (1, 2)
Kuthandiza akazi amasiye (3-16)
Kulemekeza akulu akhama (17-25)
6
Akapolo azilemekeza ambuye awo (1, 2)
Aphunzitsi onyenga ndiponso kukonda ndalama (3-10)
Malangizo kwa munthu wa Mulungu (11-16)
Kulemera pa ntchito zabwino (17-19)
Sunga zimene unalandira (20, 21)