Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g87 9/8 tsamba 31
  • Maso m’Mlengalenga

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Maso m’Mlengalenga
  • Galamukani!—1987
  • Nkhani Yofanana
  • Kuchita Zotheka Kuti Ulendo wa Pandege Ukhale Wabwino Koposa
    Galamukani!—2002
  • Zinalipo Kale M’chilengedwe
    Galamukani!—2010
  • Oona za Ndege Amakutetezani Bwanji?
    Galamukani!—2008
  • Mbalame Zimawomba Nyumba Mwangozi
    Galamukani!—2009
Onani Zambiri
Galamukani!—1987
g87 9/8 tsamba 31

Maso m’Mlengalenga

KUGUNDANA kwa mbalame ndi ndege za malonda kwakhala osati kokha kodzetsa zotaika zambiri ku makampani oyendetsa ndege komanso kwa ngozi. M’kuyesayesa kwa kufuna kuchepetsako kugundana kwa mlengalenga kumeneku, All-Nippon Airways ya ku Japan yapeza njira yatsopano ya kuwopsyera mbalame zomauluka moipa pafupi ndi ndege zawo. Motani?

Mwakulemba maso owopsya molowera mpweya mwa injini ya ndege yawo ya jeti, yadziwitsa motero magazini ya International Wildlife. Nkhaniyo inalongosola kuti eni ndege analemba maso pa 26 za ndege zawo zokhala ndi thupi lalikulu ndipo anasiya ndege zotsala zosalembedwa. Pa mapeto a kuyesa kwa chaka chimodzi, kokha avereji ya mbalame imodzi inagunda imodzi imodzi ndi imodzi ya mainjini olembedwa ndi maso owopsya. Mosiyanako, avereji ya mbalame zisanu ndi zinayi zinagunda mbali za injini zosalembedwa.

Kuwonongeka mkati mwa nthaŵi ya kuyesa kwa chaka chimodzi kunayerekezedwa kukhala $720,000, kuchoka pa $910,000. Chifukwa cha kupambana kwa kuyesaku, makonzedwe a All-Nippon Airways ali akulemba masowo pa ndege zawo zonse zokhala ndi thupi lalikulu.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena