Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g00 1/8 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Galamukani!—2000
  • Nkhani Yofanana
  • Kufunika Kowonjezereka kwa Chithandizo Ndiponso Opaleshoni Zopanda Magazi
    Galamukani!—2000
  • Opaleshoni Yopanda Kuika Magazi—Mapindu Ake Adziŵika
    Galamukani!—1998
  • Mboni za Yehova Zothandiza Kuwongolera Opaleshoni ya Mtima
    Galamukani!—1996
  • Njira Zochizira Popanda Kuika Magazi
    Galamukani!—2012
Onani Zambiri
Galamukani!—2000
g00 1/8 tsamba 1-2

Zamkatimu

January 8, 2000

Chithandizo ndi Opaleshoni Zopanda Magazi—Zikufunika Mowonjezereka

Chithandizo ndi opaleshoni zopanda magazi tsopano zafala koposa kale lonse. Kodi n’chifukwa chiyani pali ambiri ozifuna motere? Kodi ndiyo njira yabwino yoloŵa m’malo mwa kuika anthu magazi?

3 Akatswiri a Zamankhwala

4 Kuika Anthu Magazi—Nkhani Yovuta kwa Nthaŵi Yaitali

7 Kufunika Kowonjezereka kwa Chithandizo Ndiponso Opaleshoni Zopanda Magazi

12 Amayi Odwala AIDS Akusoŵa Pogwira

16 Thandizo kwa Anthu Ozunzidwa

19 Malonda a Kuba Anthu Ali Padziko Lonse

20 Kuba Anthu—Malonda Oopsa

24 Zimene Zimachititsa—Kuba Anthu

26 Kuba Anthu—Kodi Pali Njira Yokuthetsera?

32 ‘Iwo Anali Osangalatsa!’

Kuona Miyambo Yotchuka M’njira Yoyenera 14

Miyambo yambiri n’njozikidwa pa zikhulupiriro ndiponso malingaliro achipembedzo osakhala a Baibulo. Kodi Mkristu ayenera kuiona motani miyambo imeneyi?

Kodi Ndikhale ndi Khadi la Ngongole? 29

Achinyamata ayenera kulipenda mosamalitsa funso limeneli, kuona zabwino ndiponso zoipa zake zomwe.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena