Zamkatimu
November 8, 2005
Kodi Osauka Angayembekezere Zotani?
Akuti anthu okhala padziko lapansi ndi ogawikana pawiri, olemera ndi osauka. Popeza anthu osauka akuchulukirachulukira, kodi angayembekezere zotani?
3 Dziko Logawanika Chifukwa cha Chuma
4 Kusiyana Kwakukulu Pakati pa Olemera ndi Osauka
7 Njira Yeniyeni Yothetsera Umphawi
16 Zimene Achinyamata Amadzifunsa
Kodi Ndingapewe Bwanji Mavuto Pocheza ndi Anthu Osawadziwa pa Intaneti?
19 Mphamvu Zimene Manyuzipepala Ali Nazo
7 Mmene Mungapindulire ndi Manyuzipepala
27 Malo Ovuta Kuwamvetsa a ku Africa
26 Mayankho Othandiza a Mafunso Amene Mwakhala Mukufunsa
Nkhondo Imene Inasintha Moyo Wanga 11
Msilikali wa m’gulu la asilikali apamadzi wa ku United States amene anapita ku malo omenyerana nkhondo nthawi 284 pankhondo ya ku Vietnam ndipo analandira mamendulo 29 akufotokoza momwe nkhondo imeneyo inasinthira moyo wake.
Kodi Baibulo Limapondereza Akazi? 28
Anthu ambiri amati zimene Baibulo limaphunzitsa, zoti akazi azigonjera amuna n’zopondereza akazi. Kodi zimenezi n’zoona?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Cover: © Karen Robinson/Panos Pictures