Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g05 12/8 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Galamukani!—2005
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi N’chiyani Chimayambitsa Vuto la Kusowa Pokhala?
    Galamukani!—2005
  • Kodi Kusowa Pokhala Kungathe Bwanji?
    Galamukani!—2005
  • “Anthu Okhala Ngati Mfuko”
    Galamukani!—1991
  • Kusowa Pokhala Ndi Vuto la Padziko Lonse
    Galamukani!—2005
Onani Zambiri
Galamukani!—2005
g05 12/8 tsamba 1-2

Zamkatimu

December 8, 2005

Kodi Vuto la Kusowa Pokhala Lidzatha?

Kodi n’chiyani chimayambitsa vuto la padziko lonse la kuchuluka kwa anthu osowa pokhala? Kodi njira yabwino kwambiri yothandizira anthuwa ndi iti? Kodi pali chiyembekezo chilichonse chotsimikizika choti vutoli lidzatha?

3 Kusowa Pokhala Ndi Vuto la Padziko Lonse

4 Kodi N’chiyani Chimayambitsa Vuto la Kusowa Pokhala?

8 Kodi Kusowa Pokhala Kungathe Bwanji?

16 Zimene Achinyamata Amadzifunsa

Kodi Tichite Kukhala ndi Mwambo Wonse wa Ukwati?

19 Chakudya Chikatha

20 Vuto Lopezera Chakudya Anthu Okhala M’mizinda

27 Kodi Njala Idzatha Padziko Pano?

28 Sayansi ndi Baibulo Zinandithandiza Kudziwa Cholinga cha Moyo

31 Mlozera Nkhani wa Voliyumu 86 ya Galamukani!

Zilema Zanga Sizinandifooketse 11

Werengani nkhani ya mnyamata yemwe akukhala m’dziko la nkhondo ndipo akudwala matenda aakulu koma anasonyeza chikhulupiriro chosowa ndiponso kupirira kogometsa.

Kodi Mulungu Amakondera Mitundu Ina ya Anthu? 14

Anthu ambiri amakhulupirira kuti Mulungu amakonda kwambiri mtundu wawo kuposa mitundu ina, koma kodi zimenezo n’zogwirizana ndi Baibulo?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena